7 Ndipo ciwerengo cao, pamodzi ndi abale ao ophunzitsidwa ayimbire Yehova, onse anthetemya, ndiwo mazana awiri mphambu makumi asanu ndi atatu.
Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 25
Onani 1 Mbiri 25:7 nkhani