1 Mbiri 26:30 BL92

30 A Ahebroni: Hasabiya ndi abale ace odziwa mphamvu cikwi cimodzi mphambu mazana asanu ndi awiri anayang'anira Israyeli tsidya lino la Yordano kumadzulo, kuyang'anira nchito yonse ya Yehova, ndi kutumikira mfumu.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 26

Onani 1 Mbiri 26:30 nkhani