1 Mbiri 26:31 BL92

31 Yeriya ndiye mkuru wa Ahebroni, wa Ahebroni monga mwa mibadwo ya nyumba za makolo. Caka ca makumi anai ca ufumu wa Davide anafunafuna, napeza mwa iwowa ngwazi zamphamvu ku Yazeri wa ku Gileadi.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 26

Onani 1 Mbiri 26:31 nkhani