1 Mbiri 27:23 BL92

23 Koma Davide sanawerenga iwo a zaka makumi awiri ndi ocepapo, pakuti Yehova adati kuti adzacurukitsa Israyeli ngati nyenyezi za kuthambo.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 27

Onani 1 Mbiri 27:23 nkhani