1 Mbiri 27:24 BL92

24 Yoabu mwana wa Zeruya anayamba kuwerenga, koma sanatsiriza; ndi mkwiyo unagwera Israyeli cifukwa ca ici, ndipo ciwerengo cao sicinalembedwa m'buku la mbiri ya mfumu Davide.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 27

Onani 1 Mbiri 27:24 nkhani