1 Mbiri 27:28 BL92

28 ndi woyang'anira mitengo yaazitona, ndi yamikuyu yokhala kuzidikha kunsi, ndiye Baala Hanani Mgederi; ndi woyang'anira zosungiramo mafuta ndiye Yoasi;

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 27

Onani 1 Mbiri 27:28 nkhani