1 Mbiri 28:12 BL92

12 ndi cifaniziro ca zonse anali nazo mwa mzimu, ca mabwalo a nyumba ya Yehova, ndi ca zipinda zonse pozungulirapo, ca zosungiramo cuma za nyumba ya Mulungu, ndi ca zosungiramo cuma za zinthu zopatulika;

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 28

Onani 1 Mbiri 28:12 nkhani