1 Mbiri 28:17 BL92

17 ndi mitengo, ndi mbale zowazira, ndi zikho za golidi woona, ndi ca mitsuko yace yagolidi, woyesedwa kulemera kwace mtsuko uli wonse; ndi ca mitsuko yasiliva woyesedwa kulemera kwace mtsuko uli wonse;

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 28

Onani 1 Mbiri 28:17 nkhani