1 Mbiri 28:9 BL92

9 Ndipo iwe Solomo mwana wanga, umdziwe Mulungu wa atate wako, umtumikire ndi mtima wangwiro ndi moyo waufulu; pakuti Yehova asanthula mitima yonse, nazindikira zolingirira zonse za maganizo; ukamfunafuna iye udzampeza, koma ukamsiya iye adzakusiya kosatha.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 28

Onani 1 Mbiri 28:9 nkhani