1 Mbiri 29:14 BL92

14 Kama ndine yani, ndi anthu anga ndiwo ayani, kuti tidzakhoza kupereka mwaufulu motere? popeza zonsezi zifuma kwanu; takupatsani zofuma ku dzanja lanu.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 29

Onani 1 Mbiri 29:14 nkhani