1 Mbiri 29:15 BL92

15 Pakuti ife ndife alendo pamaso panu, ndi ogonera, monga makolo athu onse; masiku athu a padziko akunga mthunzi, ndipo palibe kukhalitsa.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 29

Onani 1 Mbiri 29:15 nkhani