1 Mbiri 29:18 BL92

18 Yehova Mulungu wa Abrahamu, wa Isake, ndi wa Israyeli makolo athu, musungitse ici kosatha m'cilingaliro ca maganizo a mtima wa anthu anu, nimulunjikitse mitima yao kwanu,

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 29

Onani 1 Mbiri 29:18 nkhani