1 Mbiri 29:19 BL92

19 nimupatse Solomo mwana wanga mtima wangwiro kusunga malamulo anu, mboni zanu, ndi malemba anu, ndi kucita izi zonse, ndi kumanga cinyumbaci cimene ndakonzeratu mirimo yace,

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 29

Onani 1 Mbiri 29:19 nkhani