23 Momwemo Solomo anakhala pa mpando wacifumu wa Yehova, ndiye mfumu m'malo mwa Davide atate wace, nalemerera, nammvera iye Aisrayeli onse.
Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 29
Onani 1 Mbiri 29:23 nkhani