1 Mbiri 4:2 BL92

2 Ndipo Reaya mwana wa Sobala anabala Yahati; ndi Yahati anabala Ahumai, ndi Lahadi. Iwo ndiwo mabanja a Azorati.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 4

Onani 1 Mbiri 4:2 nkhani