1 Mbiri 4:41 BL92

41 Iwo tsono olembedwa maina anadza masiku a Hezekiya mfumu ya Yuda, nakantha mahema ao ndi zokhalamo zao, naziononga konse mpaka lero, nakhala m'malo mwao; popeza panali podyetsa zoweta zao pamenepo.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 4

Onani 1 Mbiri 4:41 nkhani