1 Mbiri 4:42 BL92

42 Ndipo ena a iwowa a ana a Simeoni, amuna mazana asanu, anamka ku phiri la Seiri; akuwatsogolera ndiwo Pelatiya, ndi Neariya, ndi Refaya, ndi Uzieli; ana a lsi.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 4

Onani 1 Mbiri 4:42 nkhani