22 Pakuti adagwa, nafa ambiri, popeza nkhondoyi nja Mulungu. Ndipo anakhala m'malo mwao mpaka anatengedwa ndende.
Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 5
Onani 1 Mbiri 5:22 nkhani