21 Ndipo analanda zoweta zao, ngamila zao zikwi makumi asanu, ndi nkhosa zikwi mazana awiri ndi makumi asanu, ndi aburu zikwi ziwiri, ndi amuna zikwi zana limodzi.
Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 5
Onani 1 Mbiri 5:21 nkhani