62 Ndi kwa ana a Gerisomu monga mwa mabanja ao, motapa pa pfuko la Isakara, ndi pa pfuko la Aseri, ndi pa pfuko la Nafitali, ndi pa pfuko la Manase m'Basana, midzi khumi ndi itatu.
Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 6
Onani 1 Mbiri 6:62 nkhani