63 Ana a Merari analandira mwa maere monga mwa mabanja ao, motapa pa pfuko la Rubeni, ndi pa pfuko la Gadi, ndi pa pfuko la Zebuluni, midzi khumi ndi iwiri.
Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 6
Onani 1 Mbiri 6:63 nkhani