1 Mbiri 6:66 BL92

66 Ndi mabanja ena a ana a Kohati anali nayo midzi ya malire ao, yotapa pa pfuko la Efraimu.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 6

Onani 1 Mbiri 6:66 nkhani