4 Ndi pamodzi nao mwa mibadwo yao, mwa nyumba za makolo ao, panali magulu a nkhondo zikwi makumi atatu mphambu zisanu ndi cimodzi, popeza anacuruka akazi ao ndi ana ao.
Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 7
Onani 1 Mbiri 7:4 nkhani