1 Mbiri 7:5 BL92

5 Ndi abale ao mwa mabanja onse a Isakara, ngwazi zamphamvu, oyesedwa mwa cibadwidwe cao, onsewa ndiwo zikwi zisanu ndi zitatu mphambu zisanu ndi ziwiri.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 7

Onani 1 Mbiri 7:5 nkhani