1 Mbiri 7:40 BL92

40 Awa onse ndiwo ana a Aseri, akuru a nyumba za makolo ao, ngwazi zosankhika ndi zamphamvu, akuru mwa akalonga. Oyesedwa mwa cibadwidwe cao otumikira kunkhondo ndiwo amuna zikwi makumi awiri mphambu zisanu ndi cimodzi.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 7

Onani 1 Mbiri 7:40 nkhani