40 Ndipo ana a Ulamu ndiwo ngwazi zamphamvu, ndiwo oponya mibvi, nakhala nao ana ambiri ndi zidzukulu zana limodzi. Onsewa ndiwo a ana a Benjamini.
Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 8
Onani 1 Mbiri 8:40 nkhani