1 Mbiri 9:1 BL92

1 Ndipo Aisrayeli onse anawerengedwa mwa cibadwidwe cao; ndipo taonani, alembedwa m'buku la mafumu a Israyeli; ndipo Yuda anatengedwa ndende kumka ku Babulo cifukwa ca kulakwa kwao.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 9

Onani 1 Mbiri 9:1 nkhani