1 Mbiri 9:23 BL92

23 Momwemo iwo ndi ana ao anayang'anira zipata za ku nyumba ya Yehova, ndiyo nyumba ya kacisi, m'udikiro wao.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 9

Onani 1 Mbiri 9:23 nkhani