33 Ndipo awa ndi oyimba akuru a nyumba za makolo a Alevi, okhala m'zipinda, omasuka ku nchito zina; pakuti anali nayo nchito yao usana ndi usiku.
Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 9
Onani 1 Mbiri 9:33 nkhani