1 Mbiri 9:34 BL92

34 Awa ndi akuru a nyumba za makolo a Alevi mwa mibadwo yao, ndiwo akuru; anakhala ku Yerusalemu awa.

Werengani mutu wathunthu 1 Mbiri 9

Onani 1 Mbiri 9:34 nkhani