1 Samueli 12:10 BL92

10 Ndipo anapemphera kwa Yehova, kuti, Tinacimwa, popeza tinasiya Yehova, ndi kutumikira Abaala ndi Asitaroti, koma mutipulumutse tsopano m'manja a adani anthu, ndipo tidzakutumikirani Inu.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 12

Onani 1 Samueli 12:10 nkhani