1 Samueli 12:8 BL92

8 Pamene Yakobo anafika ku Aigupto, ndi makolo anu anapemphera kwa Yehova, Yehova anatumiza Mose ndi Aroni, amene anaturutsa makolo anu m'Aigupto, nawakhalitsa pamalo pano,

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 12

Onani 1 Samueli 12:8 nkhani