2 Ndipo Samueli anati, Ndikamuka bwanji? Sauli akacimva, adzandipha. Ndipo Yehova anati, Umuke nayo ng'ombe yaikazi, nunene kuti, Ndadza kudzaphera nsembe kwa Yehova.
Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 16
Onani 1 Samueli 16:2 nkhani