3 Ndipo uitane Jese abwere kunsembeko, ndipo Ine ndidzakusonyeza cimene uyenera kucita; ndipo udzandidzozera iye amene ndidzakuchulira dzina lace.
Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 16
Onani 1 Samueli 16:3 nkhani