1 Samueli 16:4 BL92

4 Ndipo Samueli anacita cimene Yehova ananena, nadza ku Betelehemu. Ndipo akuru a mudziwo anadza kukomana naye monthunthumira, nati, Mubwera ndi mtendere kodi?

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 16

Onani 1 Samueli 16:4 nkhani