5 Nati iye, Ndi mtendere umene; ndadza kudzaphera nsembe kwa Yehova; mudzipatule ndi kufika ndi ine kunsembeko. Ndipo iye anapatula Jese ndi ana ace, nawaitanira kunsembeko.
Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 16
Onani 1 Samueli 16:5 nkhani