1 Samueli 17:51 BL92

51 Potero Davide anathamanga naima pa Mfilistiyo, nagwira lupanga lace, nalisolola m'cimace, namtsiriza nadula nalo mutu wace. Ndipo pakuona Afilisti kuti ciwinda cao cidafa, anathawa.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 17

Onani 1 Samueli 17:51 nkhani