1 Samueli 18:22 BL92

22 Ndipo Sauli analamulira anyamata ace, nati, Mulankhule naye Davide m'tseri, ndi kuti, Taonani mfumu akondwera nanu, ndi anyamata ace onse akukondani; cifukwa cace tsono, khalani mkamwini wa mfumu.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 18

Onani 1 Samueli 18:22 nkhani