1 Samueli 24:8 BL92

8 Bwino lace Davide yemwe ananyamuka, naturuka m'phangamo, napfuulira Sauli, nati, Mbuye wanga, mfumu. Ndipo pakuceuka Sauli, Davide anaweramira nkhope yace pansi, namgwadira.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 24

Onani 1 Samueli 24:8 nkhani