1 Samueli 28:16 BL92

16 Ndip'o Samueli ananena naye, Ndipo undifunsiranji ine, popeza Yehova anakucokera, nasandulika mdani wako?

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 28

Onani 1 Samueli 28:16 nkhani