1 Samueli 28:17 BL92

17 Ndipo Yehova yekha wacita monga ananena pakamwa panga; ndipo Yehova wang'amba ufumuwo, kuucotsa m'dzanja lako, ndi kuupatsa mnansi wako, ndiye Davide.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 28

Onani 1 Samueli 28:17 nkhani