1 Samueli 4:6 BL92

6 Ndipo Afilistiwo pakumva kubuma pa kupfuula kwao, anati, Phokoso ili la kupfuula kwakukuru ku zithando za Aisrayeli litani? Ndipo anamva kuti likasa la Yehova lidzafika ku zithandozo.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 4

Onani 1 Samueli 4:6 nkhani