1 Samueli 9:1 BL92

1 Ndipo panali munthu Mbenlamlni, dzina lace ndiye Kisi, mwana wa Abiyeli, mwana wa Zerori, mwana wa Bekorati, mwana wa Afiya, mwana wa Mbenjamini, ndiye ngwazi.

Werengani mutu wathunthu 1 Samueli 9

Onani 1 Samueli 9:1 nkhani