Yobu 14:5 BL92

5 Popeza masiku ace alembedwa, ciwerengo ca miyezi yace cikhala ndi Inu,Ndipo mwamlembera malire ace, kuti asapitirirepo iye;

Werengani mutu wathunthu Yobu 14

Onani Yobu 14:5 nkhani