30 Sadzacoka mumdima;Lawi la moto lidzaumitsa nthambi zace;Ndipo adzacoka ndi mpumo wa m'kamwa mwace.
Werengani mutu wathunthu Yobu 15
Onani Yobu 15:30 nkhani