13 Ndikayembekezera kumanda kukhale nyumba yanga;Ndikayala pogona panga mumdima.
14 Ndikati kwa dzenje, Ndiwe atate wanga;Kwa mphutsi, Ndiwe mai wanga ndi mlongo wanga;
15 Ciri kuti ciyembekezo canga?Inde, ciyembekezo canga adzaciona ndani?
16 Cidzatsikira ku mipingiridzo ya kumanda,Pamene tipumulira pamodzi kupfumbi.