Yobu 2:12 BL92

12 Ndipo pokweza maso ao ali kutali, sanamdziwa, nakweza mau ao, nalira; nang'amba yense maraya ace, nawaza pfumbi kumwamba ligwe pamitu pao.

Werengani mutu wathunthu Yobu 2

Onani Yobu 2:12 nkhani