1 Koma Yobu anayankha, nati,
2 Wamthandiza bwanji wopanda mphamvu,Kulipulumutsa dzanja losalimba!
3 Wampangira bwanji wopanda nzeruyu!Ndi kudziwitsa nzeru zeni zeni mocurukal
4 Wafotokozera yani mau?Ndi mzimu wa yani unaturuka mwa iwe?
5 Adafawo anjenjemeraPansi pa madzi ndi zokhalamo,
6 Kumanda kuli padagu pamaso pace,Ndi kucionongeko kusowa cophimbako,