14 Taonani, awa ndi malekezero a njira zace;Ndi cimene tikumva za Iye ndi cinong'onezo cacing'ono;Koma kugunda kwa mphamvu yace akuzindikiritsa ndani?
Werengani mutu wathunthu Yobu 26
Onani Yobu 26:14 nkhani