Yobu 28:17 BL92

17 Golidi ndi krustalo sizilingana nayo;Ndi kusinthana kwace, siisinthanika ndi zisambiro za golidi woyengetsa.

Werengani mutu wathunthu Yobu 28

Onani Yobu 28:17 nkhani